Machitidwe 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Popeza kuti anamulamula zimenezi, iye anawaponya m’chipinda chamkati cha ndendeyo+ ndi kumanga mapazi awo m’matangadza.+
24 Popeza kuti anamulamula zimenezi, iye anawaponya m’chipinda chamkati cha ndendeyo+ ndi kumanga mapazi awo m’matangadza.+