Machitidwe 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti ndidzamuonetsa bwinobwino zopweteka zonse zimene ayenera kumva chifukwa cha dzina langa.”+ 2 Akorinto 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma tikusonyeza mwa njira ina iliyonse kuti ndife atumiki a Mulungu.+ Tikuchita zimenezi mwa kupirira zambiri, kudutsa m’masautso, kukhala osowa, kukumana ndi zovuta,+ 1 Petulo 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipotu anakuitanirani ku moyo umenewu, pakuti ngakhale Khristu anavutika chifukwa cha inu,+ ndipo anakusiyirani chitsanzo kuti mutsatire mapazi ake mosamala kwambiri.+
4 Koma tikusonyeza mwa njira ina iliyonse kuti ndife atumiki a Mulungu.+ Tikuchita zimenezi mwa kupirira zambiri, kudutsa m’masautso, kukhala osowa, kukumana ndi zovuta,+
21 Ndipotu anakuitanirani ku moyo umenewu, pakuti ngakhale Khristu anavutika chifukwa cha inu,+ ndipo anakusiyirani chitsanzo kuti mutsatire mapazi ake mosamala kwambiri.+