Mateyu 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha ndi kunyamula mtengo wake wozunzikirapo* ndipo anditsatire mosalekeza.+ Yohane 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti ndakupatsani chitsanzo kuti mmene ine ndachitira kwa inu, inunso muzichita chimodzimodzi.+
24 Kenako Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha ndi kunyamula mtengo wake wozunzikirapo* ndipo anditsatire mosalekeza.+