Mateyu 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndiponso aliyense wosalandira mtengo wake wozunzikirapo* ndi kunditsatira sali woyenera ine.+ Maliko 8:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kenako iye anaitana khamu la anthu pamodzi ndi ophunzira ake ndi kuwauza kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha ndi kunyamula mtengo wake wozunzikirapo,* ndi kunditsatira mosalekeza.+ Luka 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako anauza onse kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha+ ndi kunyamula mtengo wake wozunzikirapo* tsiku ndi tsiku ndi kunditsatira mosalekeza.+ Luka 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Aliyense wosanyamula mtengo wake wozunzikirapo* ndi kunditsatira ine sangakhale wophunzira wanga.+
34 Kenako iye anaitana khamu la anthu pamodzi ndi ophunzira ake ndi kuwauza kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha ndi kunyamula mtengo wake wozunzikirapo,* ndi kunditsatira mosalekeza.+
23 Kenako anauza onse kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha+ ndi kunyamula mtengo wake wozunzikirapo* tsiku ndi tsiku ndi kunditsatira mosalekeza.+
27 Aliyense wosanyamula mtengo wake wozunzikirapo* ndi kunditsatira ine sangakhale wophunzira wanga.+