Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 10:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Ndiponso aliyense wosalandira mtengo wake wozunzikirapo* ndi kunditsatira sali woyenera ine.+

  • Mateyu 16:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kenako Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha ndi kunyamula mtengo wake wozunzikirapo* ndipo anditsatire mosalekeza.+

  • Maliko 8:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Kenako iye anaitana khamu la anthu pamodzi ndi ophunzira ake ndi kuwauza kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha ndi kunyamula mtengo wake wozunzikirapo,* ndi kunditsatira mosalekeza.+

  • Luka 14:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Aliyense wosanyamula mtengo wake wozunzikirapo* ndi kunditsatira ine sangakhale wophunzira wanga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena