Mateyu 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndiponso aliyense wosalandira mtengo wake wozunzikirapo* ndi kunditsatira sali woyenera ine.+ Mateyu 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha ndi kunyamula mtengo wake wozunzikirapo* ndipo anditsatire mosalekeza.+ Luka 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako anauza onse kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha+ ndi kunyamula mtengo wake wozunzikirapo* tsiku ndi tsiku ndi kunditsatira mosalekeza.+ Luka 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Aliyense wosanyamula mtengo wake wozunzikirapo* ndi kunditsatira ine sangakhale wophunzira wanga.+ Agalatiya 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiponso anthu amene ali a Khristu Yesu, anapachika thupi lawo pamodzi ndi zikhumbo zake ndi zilakolako zake.+
24 Kenako Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha ndi kunyamula mtengo wake wozunzikirapo* ndipo anditsatire mosalekeza.+
23 Kenako anauza onse kuti: “Ngati munthu akufuna kunditsatira, adzikane yekha+ ndi kunyamula mtengo wake wozunzikirapo* tsiku ndi tsiku ndi kunditsatira mosalekeza.+
27 Aliyense wosanyamula mtengo wake wozunzikirapo* ndi kunditsatira ine sangakhale wophunzira wanga.+
24 Ndiponso anthu amene ali a Khristu Yesu, anapachika thupi lawo pamodzi ndi zikhumbo zake ndi zilakolako zake.+