Machitidwe 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atakhala kumeneko miyezi itatu, anaganiza zobwerera ku Makedoniya, chifukwa chakuti Ayuda+ anamukonzera chiwembu. Chiwembuchi anachikonza Paulo atangotsala pangʼono kuyamba ulendo wapamadzi wopita ku Siriya. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:3 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 167-168 Nsanja ya Olonda,3/15/2001, tsa. 316/15/1990, tsa. 21
3 Atakhala kumeneko miyezi itatu, anaganiza zobwerera ku Makedoniya, chifukwa chakuti Ayuda+ anamukonzera chiwembu. Chiwembuchi anachikonza Paulo atangotsala pangʼono kuyamba ulendo wapamadzi wopita ku Siriya.