1 Samueli 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuyambira tsiku limenelo, Sauli anayamba kuyang’ana Davide ndi diso loipa.+ Miyambo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mkwiyo umasefukira ndipo ukali ndi wankhanza,+ koma nsanje ndani angaipirire?+ Yakobo 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 chifukwa mkwiyo wa munthu subala chilungamo cha Mulungu.+