Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 37:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Abale akewo anachita naye kaduka,+ koma bambo ake anasunga mawuwo.+

  • Miyambo 14:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Mtima wodekha ndiwo moyo wa munthu,+ koma nsanje imawoletsa mafupa.+

  • Machitidwe 17:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma Ayuda anachita nsanje,+ ndipo anatengana ndi anthu ena oipa, anthu osowa chochita amene anali kungokhala pamsika. Iwowa anapanga gulu lachiwawa ndi kuyambitsa chipolowe mumzindamo.+ Kenako anakhamukira kunyumba ya Yasoni,+ kukafuna atumwiwo kuti awatulutsire ku gulu lachipolowelo.

  • Yakobo 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma ngati m’mitima mwanu muli nsanje yaikulu+ ndi kukonda mikangano,+ musadzitamande+ pakuti kutero n’kunamizira choonadi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena