Genesis 37:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Abale ake ataona kuti bambo awo anali kum’konda kwambiri Yosefe kuposa iwo onse, anayamba kudana naye,+ moti sankatha kulankhula naye mwamtendere.+ 1 Samueli 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Sauli atamva zimenezi anakwiya kwambiri+ ndipo mawu amenewa anamuipira, moti anayamba kuganiza kuti: “Davide amupatsa masauzande makumimakumi, koma ine angondipatsa masauzande okha. Ndiye kuti kwangotsala kum’patsa ufumuwu basi!”+
4 Abale ake ataona kuti bambo awo anali kum’konda kwambiri Yosefe kuposa iwo onse, anayamba kudana naye,+ moti sankatha kulankhula naye mwamtendere.+
8 Sauli atamva zimenezi anakwiya kwambiri+ ndipo mawu amenewa anamuipira, moti anayamba kuganiza kuti: “Davide amupatsa masauzande makumimakumi, koma ine angondipatsa masauzande okha. Ndiye kuti kwangotsala kum’patsa ufumuwu basi!”+