-
Genesis 37:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Abale ake ataona kuti bambo awo ankakonda kwambiri Yosefe kuposa abale ake onse, anayamba kudana naye, moti sankalankhula naye mwamtendere.
-