Genesis 37:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Abale ake ataona kuti bambo awo anali kum’konda kwambiri Yosefe kuposa iwo onse, anayamba kudana naye,+ moti sankatha kulankhula naye mwamtendere.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:4 Nsanja ya Olonda,8/1/2014, ptsa. 12-13
4 Abale ake ataona kuti bambo awo anali kum’konda kwambiri Yosefe kuposa iwo onse, anayamba kudana naye,+ moti sankatha kulankhula naye mwamtendere.+