Miyambo 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mtima wodekha ndiwo moyo wa munthu,+ koma nsanje imawoletsa mafupa.+ Miyambo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mkwiyo umasefukira ndipo ukali ndi wankhanza,+ koma nsanje ndani angaipirire?+