Agalatiya 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 kupembedza mafano, kuchita zamizimu,+ udani, ndewu, nsanje, kupsa mtima, mikangano, kugawikana, magulu ampatuko, Tito 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ngakhale ife nthawi inayake tinali opanda nzeru, osamvera, osocheretsedwa, akapolo a zilakolako ndi zosangalatsa zosiyanasiyana, ochita zoipa, akaduka, onyansa ndiponso achidani.+
20 kupembedza mafano, kuchita zamizimu,+ udani, ndewu, nsanje, kupsa mtima, mikangano, kugawikana, magulu ampatuko,
3 Pakuti ngakhale ife nthawi inayake tinali opanda nzeru, osamvera, osocheretsedwa, akapolo a zilakolako ndi zosangalatsa zosiyanasiyana, ochita zoipa, akaduka, onyansa ndiponso achidani.+