Genesis 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 koma sanakondwere naye Kaini ndi nsembe yake+ m’pang’ono pomwe. Chotero Kaini anapsa mtima kwambiri+ ndipo nkhope yake inagwa. Miyambo 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mtima wodekha ndiwo moyo wa munthu,+ koma nsanje imawoletsa mafupa.+ Miyambo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mkwiyo umasefukira ndipo ukali ndi wankhanza,+ koma nsanje ndani angaipirire?+ Yakobo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti pamene pali nsanje+ ndi mtima wokonda mikangano, palinso chisokonezo ndi zoipa zamtundu uliwonse.+
5 koma sanakondwere naye Kaini ndi nsembe yake+ m’pang’ono pomwe. Chotero Kaini anapsa mtima kwambiri+ ndipo nkhope yake inagwa.
16 Pakuti pamene pali nsanje+ ndi mtima wokonda mikangano, palinso chisokonezo ndi zoipa zamtundu uliwonse.+