Miyambo 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mtima wodekha ndiwo moyo wa munthu,+ koma nsanje imawoletsa mafupa.+