Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 17
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Machitidwe 17:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1At 2:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 133

Machitidwe 17:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 9:20; 13:14; 14:1; 18:4
  • +Mac 18:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 134-135

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/2012, tsa. 19

    12/1/2008, tsa. 30

    3/1/1986, tsa. 29

    Sukulu ya Utumiki, ptsa. 251-252

Machitidwe 17:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 22:7, 16; 34:20; 69:21; 118:22; Yes 50:6; 53:3, 5
  • +Sl 16:10; Lu 24:46
  • +Mac 18:28; Aga 3:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 134-135

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/2012, tsa. 19

    12/1/2008, tsa. 30

    6/15/1990, ptsa. 17-18

    Galamukani!,

    4/8/1993, tsa. 21

Machitidwe 17:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 28:24
  • +Mac 15:22, 40

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 135

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/2012, tsa. 19

    11/1/1997, tsa. 11

Machitidwe 17:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:45
  • +Mac 16:20
  • +Aro 16:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 135-136, 139

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/2012, tsa. 19

Machitidwe 17:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Mf 18:17; Mac 16:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 135-136

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/2012, ptsa. 19-20

    6/1/1993, tsa. 3

Machitidwe 17:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eza 4:12
  • +Lu 23:2; Yoh 19:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 135-136

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/2012, tsa. 20

Machitidwe 17:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 136

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/2012, tsa. 20

Machitidwe 17:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 9:25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 136-137

Machitidwe 17:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 16:29
  • +Yoh 5:39
  • +Miy 14:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 137-138

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 2

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2011, tsa. 25

    4/15/2007, ptsa. 14-15

    10/15/1998, tsa. 6

    5/15/1996, ptsa. 16-17

    8/15/1990, tsa. 29

    6/15/1990, tsa. 18

    8/1/1989, tsa. 6

    1/15/1989, tsa. 6

    Galamukani!,

    3/2008, ptsa. 8-9

    8/2007, ptsa. 10-11

    10/8/1991, ptsa. 12-13

Machitidwe 17:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:50

Machitidwe 17:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 14:19; 1At 2:15
  • +Mac 14:2

Machitidwe 17:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 10:23

Machitidwe 17:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 16:1; 1At 3:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/2004, tsa. 19

    6/15/1990, tsa. 18

Machitidwe 17:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Pe 2:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 140

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/1998, ptsa. 26-27

    2/15/1989, tsa. 5

Machitidwe 17:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:5; 18:19
  • +Miy 1:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 140-141

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 18

Machitidwe 17:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 1:22; Akl 2:8
  • +1Ak 4:13
  • +Yoh 5:29; 11:25; 1Ak 15:12; Chv 20:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 141-142

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2003, tsa. 22

    8/1/2001, tsa. 8

    7/15/1998, ptsa. 25, 27

    6/15/1990, tsa. 18

    6/15/1989, tsa. 4

    2/15/1989, ptsa. 5-6

Machitidwe 17:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mko 1:27

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2137

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/1990, tsa. 18

    2/15/1989, ptsa. 5-6

Machitidwe 17:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 2:12

Machitidwe 17:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Galamukani!,

    3/2011, tsa. 18

Machitidwe 17:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 17:34
  • +Mac 17:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Muzikonda Anthu, lesson 5

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 142-143

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2010, tsa. 30

    9/1/2007, tsa. 14

    2/15/1989, ptsa. 6-7

    3/1/1986, tsa. 30

    Sukulu ya Utumiki, tsa. 252

Machitidwe 17:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Muzikonda Anthu, lesson 5

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 143

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2012, tsa. 18

    7/15/2010, tsa. 30

    7/15/2002, tsa. 32

    2/15/1989, ptsa. 6-7

    Galamukani!,

    3/2011, tsa. 18

    Mawu a Mulungu, tsa. 64

Machitidwe 17:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Mf 8:27; Yes 66:1; Mac 7:48
  • +Sl 146:6; Yes 42:5; Mac 4:24; 14:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 144

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2010, tsa. 30

    7/1/2008, tsa. 10

    2/15/1989, ptsa. 7-8

Machitidwe 17:25

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 50:12
  • +Ge 2:7
  • +Yes 42:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 144

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 38

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2010, tsa. 30

    7/1/2008, tsa. 10

    2/15/1989, ptsa. 7-8

Machitidwe 17:26

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 5:2
  • +Ge 1:28
  • +De 32:8
  • +Sl 74:17
  • +De 2:5, 19; 32:8; Yes 34:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri, article 64

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 144-145

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2010, tsa. 30

    7/1/2008, tsa. 10

    9/15/1998, ptsa. 11-12

    6/15/1990, tsa. 18

    2/15/1989, ptsa. 8-9

    5/15/1988, tsa. 10

    Buku la Onse, ptsa. 24-25

    Galamukani!,

    9/8/1993, tsa. 9

Machitidwe 17:27

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 4:29; Yes 55:6
  • +Sl 145:18; Yer 23:23; Aro 1:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 145

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2010, tsa. 30

    7/1/2008, tsa. 10

    2/15/1989, tsa. 9

Machitidwe 17:28

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 42:5
  • +Tit 1:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 146

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 38

    Galamukani!,

    3/2011, tsa. 18

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2010, ptsa. 30-31

    6/15/2004, tsa. 14

    2/15/1989, ptsa. 9-10

    3/1/1986, tsa. 30

Machitidwe 17:29

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 1:27
  • +Yos 22:22; Sl 50:1; Yes 46:9
  • +De 5:8; Yes 37:19; 40:18; 46:5; Mac 19:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 146

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2010, ptsa. 30-31

    1/15/2004, tsa. 32

Machitidwe 17:30

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 14:16; Aro 3:25; 5:13; Aef 4:18
  • +Lu 24:47

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 146-147

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2010, tsa. 31

    7/1/1992, tsa. 32

    2/15/1989, ptsa. 10-11

Machitidwe 17:31

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 96:13; 98:9; Yes 2:4; Yoh 5:22; Mac 10:42
  • +Yoh 11:25; Mac 2:24; 13:33; Aro 6:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 147

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2010, tsa. 31

    1/15/2008, tsa. 20

    7/1/1992, tsa. 32

    6/15/1990, tsa. 18

    6/15/1989, tsa. 7

    2/15/1989, ptsa. 11-15

    3/1/1987, tsa. 32

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 296

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 175

Machitidwe 17:32

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 1:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 147

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2010, tsa. 31

    7/1/1998, tsa. 12

Machitidwe 17:34

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 17:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2010, tsa. 31

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Mac. 17:11At 2:1
Mac. 17:2Mac 9:20; 13:14; 14:1; 18:4
Mac. 17:2Mac 18:19
Mac. 17:3Sl 22:7, 16; 34:20; 69:21; 118:22; Yes 50:6; 53:3, 5
Mac. 17:3Sl 16:10; Lu 24:46
Mac. 17:3Mac 18:28; Aga 3:1
Mac. 17:4Mac 28:24
Mac. 17:4Mac 15:22, 40
Mac. 17:5Mac 13:45
Mac. 17:5Mac 16:20
Mac. 17:5Aro 16:21
Mac. 17:61Mf 18:17; Mac 16:20
Mac. 17:7Eza 4:12
Mac. 17:7Lu 23:2; Yoh 19:12
Mac. 17:10Mac 9:25
Mac. 17:11Lu 16:29
Mac. 17:11Yoh 5:39
Mac. 17:11Miy 14:15
Mac. 17:12Mac 13:50
Mac. 17:13Mac 14:19; 1At 2:15
Mac. 17:13Mac 14:2
Mac. 17:14Mt 10:23
Mac. 17:15Mac 16:1; 1At 3:2
Mac. 17:162Pe 2:8
Mac. 17:17Mac 13:5; 18:19
Mac. 17:17Miy 1:20
Mac. 17:181Ak 1:22; Akl 2:8
Mac. 17:181Ak 4:13
Mac. 17:18Yoh 5:29; 11:25; 1Ak 15:12; Chv 20:6
Mac. 17:19Mko 1:27
Mac. 17:20Mac 2:12
Mac. 17:22Mac 17:34
Mac. 17:22Mac 17:16
Mac. 17:241Mf 8:27; Yes 66:1; Mac 7:48
Mac. 17:24Sl 146:6; Yes 42:5; Mac 4:24; 14:15
Mac. 17:25Sl 50:12
Mac. 17:25Ge 2:7
Mac. 17:25Yes 42:5
Mac. 17:26Ge 5:2
Mac. 17:26Ge 1:28
Mac. 17:26De 32:8
Mac. 17:26Sl 74:17
Mac. 17:26De 2:5, 19; 32:8; Yes 34:17
Mac. 17:27De 4:29; Yes 55:6
Mac. 17:27Sl 145:18; Yer 23:23; Aro 1:20
Mac. 17:28Yes 42:5
Mac. 17:28Tit 1:12
Mac. 17:29Ge 1:27
Mac. 17:29Yos 22:22; Sl 50:1; Yes 46:9
Mac. 17:29De 5:8; Yes 37:19; 40:18; 46:5; Mac 19:26
Mac. 17:30Mac 14:16; Aro 3:25; 5:13; Aef 4:18
Mac. 17:30Lu 24:47
Mac. 17:31Sl 96:13; 98:9; Yes 2:4; Yoh 5:22; Mac 10:42
Mac. 17:31Yoh 11:25; Mac 2:24; 13:33; Aro 6:5
Mac. 17:321Ak 1:23
Mac. 17:34Mac 17:19
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
  • 28
  • 29
  • 30
  • 31
  • 32
  • 33
  • 34
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Machitidwe 17:1-34

Machitidwe

17 Iwo tsopano anayenda kudutsa ku Amfipoli ndi ku Apoloniya ndipo anafika ku Tesalonika,+ kumene kunali sunagoge wa Ayuda. 2 Choncho mwachizolowezi chake,+ Paulo analowa m’sunagogemo, ndipo kwa masabata atatu anakambirana nawo mfundo za m’Malemba.+ 3 Iye anali kufotokoza ndi kusonyeza umboni wolembedwa powatsimikizira kuti kunali koyenera kuti Khristu avutike+ ndi kuuka kwa akufa.+ Anali kunena kuti: “Yesu amene ndikumulalikira kwa inu, ndiye Khristu.”+ 4 Zotsatira zake, ena mwa iwo anakhala okhulupirira+ ndipo anagwirizana ndi Paulo ndi Sila.+ Ndipo khamu lalikulu la Agiriki opembedza Mulungu, ndi amayi ambiri olemekezeka anachitanso chimodzimodzi.

5 Koma Ayuda anachita nsanje,+ ndipo anatengana ndi anthu ena oipa, anthu osowa chochita amene anali kungokhala pamsika. Iwowa anapanga gulu lachiwawa ndi kuyambitsa chipolowe mumzindamo.+ Kenako anakhamukira kunyumba ya Yasoni,+ kukafuna atumwiwo kuti awatulutsire ku gulu lachipolowelo. 6 Atalephera kuwapeza, anakokera Yasoni ndi abale ena kwa olamulira a mzindawo, akufuula kuti: “Anthu awa amene abweretsa mavuto+ padziko lapansi kumene kuli anthu, tsopano akupezekanso kuno, 7 ndipo Yasoni anawalandira bwino. Anthu onsewa akuchita zotsutsana ndi malamulo+ a Kaisara. Akunena kuti eti kulinso mfumu ina+ dzina lake Yesu.” 8 Ndi mawu amenewa, iwo anautsa mkwiyo wa khamu la anthu lija ndi olamulira a mzindawo. 9 Pamenepo olamulira a mzindawo analipiritsa Yasoni ndi enawo ndalama, kenako anawamasula.

10 Kutangoda,+ abale anatulutsa Paulo ndi Sila ndi kuwatumiza ku Bereya. Iwo atafika kumeneko, analowa m’sunagoge wa Ayuda. 11 Koma anthu a ku Bereya anali a mtima wofuna kuphunzira kuposa a ku Tesalonika aja. Iwowa analandira mawu a Mulungu ndi chidwi chachikulu kwambiri, ndipo tsiku ndi tsiku anali kufufuza+ Malemba+ mosamala kuti atsimikizire ngati zimene anamvazo zinalidi zoona.+ 12 Chotero ambiri a iwo anakhala okhulupirira, chimodzimodzinso akazi ndi amuna ambiri otchuka+ achigiriki. 13 Koma Ayuda ochokera ku Tesalonika atamva kuti Paulo akufalitsanso mawu a Mulungu ku Bereya, anapitanso kumeneko kukayambitsa chipolowe+ ndi kuchititsa anthuwo kukwiyira+ atumwiwo. 14 Nthawi yomweyo abale anatumiza Paulo kuti apite kunyanja.+ Koma Sila ndi Timoteyo anatsalira kumeneko. 15 Ndipo anthu amene anaperekeza Paulo anakamufikitsa ku Atene. Koma anabwerera atatumidwa kuti akauze Sila ndi Timoteyo+ kuti amutsatire msanga.

16 Pamene Paulo anali kuwayembekezera ku Atene, mtima unamuwawa kwambiri+ poona kuti mumzindawo mwadzaza mafano. 17 Choncho ali m’sunagoge anayamba kukambirana ndi Ayuda+ ndi anthu ena opembedza Mulungu. Ndipo tsiku ndi tsiku analinso kukambirana ndi anthu amene anali kuwapeza pamsika.+ 18 Koma ena anzeru za dziko, Aepikureya ndi Asitoiki+ anayamba kutsutsana naye. Ndipo ena anali kunena kuti: “Kodi nayenso wobwetuka uyu akufuna kunena chiyani?”+ Enanso anali kunena kuti: “Akuoneka kuti ndi wofalitsa za milungu yachilendo.” Ananena zimenezi chifukwa chakuti Paulo anali kulengeza uthenga wabwino wa Yesu ndi za kuuka kwa akufa.+ 19 Choncho anamugwira n’kupita naye kubwalo la Areopagi, ndi kunena kuti: “Kodi tingadziweko za chiphunzitso chatsopanochi+ chimene iwe ukuphunzitsa? 20 Chifukwatu zimene ukufotokozazi ndi zinthu zachilendo m’makutu mwathu. Choncho tikufuna tidziwe tanthauzo la zimenezi.”+ 21 Ndipotu nzika zonse za mu Atene ndi alendo ogonera kumeneko, anali kuthera nthawi yawo yonse yopuma akufotokoza kapena kumvetsera nkhani yatsopano. 22 Tsopano Paulo anaimirira pakati pa bwalo la Areopagi+ ndi kunena kuti:

“Amuna inu a mu Atene, ndaona kuti pa zinthu zonse mumaopa kwambiri milungu+ kuposa mmene ena amachitira. 23 Mwachitsanzo, pamene ndinali kudutsa ndi kuyang’anitsitsa zinthu zimene mumalambira, ndapezanso guwa lansembe lolembedwa kuti ‘Kwa Mulungu Wosadziwika.’ Chotero ine ndikulalikira kwa inu za Mulungu wosadziwika amene mukumulambirayo. 24 Mulungu amene anapanga dzikoli ndi zinthu zonse zili mmenemu, sakhala mu akachisi opangidwa ndi manja.+ Iye ndiye Ambuye wakumwamba ndi dziko lapansi.+ 25 Komanso satumikiridwa ndi manja a anthu ngati kuti amasowa kanthu,+ chifukwa ndi iyeyo amene amapatsa anthu onse moyo,+ mpweya,+ ndi zinthu zonse. 26 Ndipo kuchokera mwa munthu mmodzi+ anapanga mtundu wonse wa anthu,+ kuti akhale padziko lonse lapansi.+ Iye anakhazikitsa nthawi zoikidwiratu+ komanso anaika malire achikhalire a malo oti anthu azikhala.+ 27 Anachita zimenezi kuti anthuwo afunefune Mulungu,+ amufufuzefufuze ndi kumupezadi,+ ngakhale kuti kwenikweni, iye sali kutali ndi aliyense wa ife. 28 Pakuti chifukwa cha iye tili ndi moyo, timayenda ndipo tilipo,+ monga mmene andakatulo+ ena pakati panu anenera kuti, ‘Pakuti ndife mbadwa zake.’

29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+ 30 Zoona, Mulungu analekerera nthawi ya kusadziwa koteroko,+ koma tsopano akuuza anthu kwina kulikonse kuti onse alape.+ 31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.”

32 Ndiyeno anthuwo atamva za kuuka kwa akufa, ena anayamba kuseka monyodola,+ pamene ena anati: “Chabwino, udzatiuzenso zimenezi nthawi ina.” 33 Choncho Paulo anachoka pakati pawo. 34 Koma anthu ena anakhala kumbali yake ndipo anakhala otsatira a Yesu. Ena mwa iwo anali Diyonisiyo, woweruza m’bwalo la Areopagi,+ mayi wina dzina lake Damarisi ndi ena ambiri.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena