Machitidwe 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atafika kumeneko, mumzinda wa Salami anayamba kufalitsa mawu a Mulungu m’masunagoge a Ayuda. Iwo analinso ndi Yohane+ monga wowatumikira. Machitidwe 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho onse anafika ku Efeso, ndipo anzakewo anawasiya kumeneko. Koma iye yekha analowa m’sunagoge+ ndi kuyamba kukambirana ndi Ayuda.
5 Atafika kumeneko, mumzinda wa Salami anayamba kufalitsa mawu a Mulungu m’masunagoge a Ayuda. Iwo analinso ndi Yohane+ monga wowatumikira.
19 Choncho onse anafika ku Efeso, ndipo anzakewo anawasiya kumeneko. Koma iye yekha analowa m’sunagoge+ ndi kuyamba kukambirana ndi Ayuda.