Machitidwe 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anapitiriza ulendo wawo kuchokera ku Pega ndi kukafika ku Antiokeya wa ku Pisidiya. Kumeneko analowa m’sunagoge+ tsiku la sabata ndi kukhala pansi. Machitidwe 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho mwachizolowezi chake,+ Paulo analowa m’sunagogemo, ndipo kwa masabata atatu anakambirana nawo mfundo za m’Malemba.+
14 Iwo anapitiriza ulendo wawo kuchokera ku Pega ndi kukafika ku Antiokeya wa ku Pisidiya. Kumeneko analowa m’sunagoge+ tsiku la sabata ndi kukhala pansi.
2 Choncho mwachizolowezi chake,+ Paulo analowa m’sunagogemo, ndipo kwa masabata atatu anakambirana nawo mfundo za m’Malemba.+