Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 16:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsiku la sabata tinatuluka pachipata n’kupita m’mbali mwa mtsinje, kumene tinali kuganiza kuti kuli malo opempherera. Ndiyeno tinakhala pansi ndi kuyamba kulankhula ndi amayi amene anali atasonkhana kumeneko.

  • Machitidwe 17:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho mwachizolowezi chake,+ Paulo analowa m’sunagogemo, ndipo kwa masabata atatu anakambirana nawo mfundo za m’Malemba.+

  • Machitidwe 18:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Komabe Paulo anali kukamba nkhani m’sunagoge+ sabata lililonse, ndipo anali kukopa Ayuda ndi Agiriki.

  • Machitidwe 19:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kwa miyezi itatu, anali kupita kusunagoge+ kumene anali kulankhula molimba mtima. Kumeneko anali kukamba nkhani ndi kuwafotokozera mfundo zokhutiritsa zokhudza ufumu+ wa Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena