Luka 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako anabwera ku Nazareti,+ kumene analeredwa. Malinga ndi chizolowezi chake pa tsiku la sabata, analowa m’sunagoge,+ ndi kuimirira kuti awerenge Malemba. Machitidwe 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atafika kumeneko, mumzinda wa Salami anayamba kufalitsa mawu a Mulungu m’masunagoge a Ayuda. Iwo analinso ndi Yohane+ monga wowatumikira. Machitidwe 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho mwachizolowezi chake,+ Paulo analowa m’sunagogemo, ndipo kwa masabata atatu anakambirana nawo mfundo za m’Malemba.+
16 Kenako anabwera ku Nazareti,+ kumene analeredwa. Malinga ndi chizolowezi chake pa tsiku la sabata, analowa m’sunagoge,+ ndi kuimirira kuti awerenge Malemba.
5 Atafika kumeneko, mumzinda wa Salami anayamba kufalitsa mawu a Mulungu m’masunagoge a Ayuda. Iwo analinso ndi Yohane+ monga wowatumikira.
2 Choncho mwachizolowezi chake,+ Paulo analowa m’sunagogemo, ndipo kwa masabata atatu anakambirana nawo mfundo za m’Malemba.+