16Choncho Paulo anafika ku Debe ndiponso ku Lusitara.+ Kumeneko kunali wophunzira wina dzina lake Timoteyo,+ mwana wa mayi wachiyuda wokhulupirira, koma bambo ake anali Mgiriki.
2 Chotero tinatumiza Timoteyo+ m’bale wathu ndi mtumiki wa Mulungu pa uthenga wabwino+ wonena za Khristu, kuti adzakulimbitseni ndi kukutonthozani pa chikhulupiriro chanu,