Machitidwe 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iwo atadziwitsidwa zimenezi, anathawira+ m’mizinda ya Lukaoniya, Lusitara, Debe, ndi m’madera ozungulira. 2 Timoteyo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ukudziwanso mazunzo ndi masautso amene ndinakumana nawo ku Antiokeya,+ ku Ikoniyo,+ ndi ku Lusitara.+ Komabe, Ambuye anandipulumutsa m’mazunzo onsewa.+
6 Koma iwo atadziwitsidwa zimenezi, anathawira+ m’mizinda ya Lukaoniya, Lusitara, Debe, ndi m’madera ozungulira.
11 Ukudziwanso mazunzo ndi masautso amene ndinakumana nawo ku Antiokeya,+ ku Ikoniyo,+ ndi ku Lusitara.+ Komabe, Ambuye anandipulumutsa m’mazunzo onsewa.+