Machitidwe 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno anthu a mitundu ina komanso Ayuda pamodzi ndi olamulira awo, anakonza chiwembu kuti achitire chipongwe atumwiwo ndi kuwaponya miyala.+
5 Ndiyeno anthu a mitundu ina komanso Ayuda pamodzi ndi olamulira awo, anakonza chiwembu kuti achitire chipongwe atumwiwo ndi kuwaponya miyala.+