22 Choncho ku Makedoniya anatumizako awiri mwa anthu amene anali kumutumikira, omwe ndi Timoteyo+ ndi Erasito.+ Koma iye anatsalira m’chigawo cha Asia kwa kanthawi ndithu.
2 Chotero tinatumiza Timoteyo+ m’bale wathu ndi mtumiki wa Mulungu pa uthenga wabwino+ wonena za Khristu, kuti adzakulimbitseni ndi kukutonthozani pa chikhulupiriro chanu,