Machitidwe 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Paulo anafika ku Debe ndiponso ku Lusitara.+ Kumeneko kunali wophunzira wina dzina lake Timoteyo,+ mwana wa mayi wachiyuda wokhulupirira, koma bambo ake anali Mgiriki. Afilipi 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma ine, mwa Ambuye Yesu ndikuyembekeza kutumiza Timoteyo kwa inu posachedwapa, kuti ndidzasangalale+ ndikadzamva mmene zinthu zilili kwa inu.
16 Choncho Paulo anafika ku Debe ndiponso ku Lusitara.+ Kumeneko kunali wophunzira wina dzina lake Timoteyo,+ mwana wa mayi wachiyuda wokhulupirira, koma bambo ake anali Mgiriki.
19 Koma ine, mwa Ambuye Yesu ndikuyembekeza kutumiza Timoteyo kwa inu posachedwapa, kuti ndidzasangalale+ ndikadzamva mmene zinthu zilili kwa inu.