1 Atesalonika 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiye tinatumiza Timoteyo+ mʼbale wathu, yemwe ndi mtumiki wa Mulungu* amene akulengeza uthenga wabwino wonena za Khristu. Tinamutumiza kuti adzakulimbikitseni ndi kukutonthozani nʼcholinga choti chikhulupiriro chanu chikhale cholimba. 1 Atesalonika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:2 Nsanja ya Olonda,5/15/2009, tsa. 1410/1/1986, ptsa. 10-23
2 Ndiye tinatumiza Timoteyo+ mʼbale wathu, yemwe ndi mtumiki wa Mulungu* amene akulengeza uthenga wabwino wonena za Khristu. Tinamutumiza kuti adzakulimbikitseni ndi kukutonthozani nʼcholinga choti chikhulupiriro chanu chikhale cholimba.