Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 16:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kenako Paulo anafika ku Debe ndiponso ku Lusitara.+ Kumeneko kunali wophunzira wina dzina lake Timoteyo,+ mwana wa mayi wa Chiyuda wokhulupirira, koma bambo ake anali Mgiriki. 2 Abale a ku Lusitara ndi ku Ikoniyo anapereka umboni wabwino wonena za iyeyo.

  • Aroma 16:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Wantchito mnzanga Timoteyo akupereka moni, chimodzimodzinso Lukiyo, Yasoni ndi Sosipato omwe ndi achibale anga.+

  • 1 Akorinto 16:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Timoteyo+ akadzafika mudzaonetsetse kuti asadzakhale ndi mantha pakati panu, chifukwa iye akugwira ntchito ya Yehova,*+ ngati mmene inenso ndikuchitira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena