Machitidwe 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Paulo anafika ku Debe ndiponso ku Lusitara.+ Kumeneko kunali wophunzira wina dzina lake Timoteyo,+ mwana wa mayi wachiyuda wokhulupirira, koma bambo ake anali Mgiriki. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:1 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 122 Nsanja ya Olonda,11/1/2015, tsa. 96/15/1990, tsa. 14
16 Choncho Paulo anafika ku Debe ndiponso ku Lusitara.+ Kumeneko kunali wophunzira wina dzina lake Timoteyo,+ mwana wa mayi wachiyuda wokhulupirira, koma bambo ake anali Mgiriki.