Machitidwe 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atalephera kuwapeza, anakokera Yasoni ndi abale ena kwa olamulira a mzindawo, akufuula kuti: “Anthu awa, amene ayambitsa mavuto kwina konseku, tsopano akupezekanso kuno.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:6 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 135-136 Nsanja ya Olonda,6/1/2012, ptsa. 19-206/1/1993, tsa. 3
6 Atalephera kuwapeza, anakokera Yasoni ndi abale ena kwa olamulira a mzindawo, akufuula kuti: “Anthu awa, amene ayambitsa mavuto kwina konseku, tsopano akupezekanso kuno.+
17:6 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 135-136 Nsanja ya Olonda,6/1/2012, ptsa. 19-206/1/1993, tsa. 3