Mateyu 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Akakuzunzani mumzinda wina, muthawire mumzinda wina,+ pakuti ndithu ndikukuuzani, simudzamaliza kuzungulira+ mizinda yonse ya Isiraeli Mwana wa munthu asanafike.+
23 Akakuzunzani mumzinda wina, muthawire mumzinda wina,+ pakuti ndithu ndikukuuzani, simudzamaliza kuzungulira+ mizinda yonse ya Isiraeli Mwana wa munthu asanafike.+