Mateyu 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Akakuzunzani mumzinda umodzi, muthawire mumzinda wina.+ Ndithu ndikukuuzani, simudzamaliza kuzungulira mizinda yonse ya Isiraeli Mwana wa munthu asanafike. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:23 Yesu—Ndi Njira, tsa. 124 Nsanja ya Olonda,4/15/2002, tsa. 328/1/1987, ptsa. 28-29
23 Akakuzunzani mumzinda umodzi, muthawire mumzinda wina.+ Ndithu ndikukuuzani, simudzamaliza kuzungulira mizinda yonse ya Isiraeli Mwana wa munthu asanafike.