Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 16:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndithu ndikukuuzani kuti pali ena mwa amene aimirira pano amene sadzalawa imfa m’pang’ono pomwe kufikira choyamba ataona Mwana wa munthu akubwera monga mfumu.”+

  • Mateyu 24:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Uthenga wabwino+ uwu wa ufumu+ udzalalikidwa padziko lonse lapansi kumene kuli anthu, kuti ukhale umboni ku mitundu yonse,+ kenako mapeto+ adzafika.

  • Aroma 10:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma ndifunsebe kuti, Kodi kumva sanamve? Pajatu “liwu lawo linamveka padziko lonse lapansi,+ ndipo mawu awo anamveka kumalekezero a dziko lapansi kumene kuli anthu.”+

  • Akolose 1:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Adzaterodi, malinga ngati mupitirizabe m’chikhulupiriro,+ muli okhazikika pamaziko+ ndiponso olimba, osasunthika+ pa chiyembekezo cha uthenga wabwino umene munamva,+ umenenso unalalikidwa+ m’chilengedwe chonse+ cha pansi pa thambo. Uthenga wabwino umenewu ndi umene ineyo Paulo ndinakhala mtumiki wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena