Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 11:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndi atumiki a Khristu kapena? Ndikuyankha ngati wamisala, ineyo ndiye weniweni woposanso iwowo:+ m’ntchito zovuta mowirikiza koposa,+ m’ndende osachita kunena,+ kumenyedwa kosawerengeka, kutsala pang’ono kufa kawirikawiri.+

  • Aefeso 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kukoma mtima kwakukulu kumeneku kunapatsidwa kwa ine, munthu wochepa pondiyerekeza ndi wochepetsetsa+ wa oyera onse. Ndinapatsidwa kukoma mtima kumeneku+ kuti ndilengeze kwa mitundu ina+ uthenga wabwino wonena za chuma chopanda polekezera+ cha Khristu,

  • 2 Timoteyo 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Uthenga wabwino umenewu ndi umene anandiikira kuti ndikhale mlaliki, mtumwi ndi mphunzitsi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena