1 Akorinto 15:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Choncho abale anga okondedwa, khalani olimba,+ osasunthika, okhala ndi zochita zambiri nthawi zonse mu ntchito ya Ambuye,+ podziwa kuti zonse zimene mukuchita mu ntchito ya Ambuye sizidzapita pachabe.+ Aheberi 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti kwenikweni timachita nawo zimene Khristu akuchita,+ ngati zinthu zimene tinali kudalira pa chiyambi, tazigwira mwamphamvu mpaka mapeto.+
58 Choncho abale anga okondedwa, khalani olimba,+ osasunthika, okhala ndi zochita zambiri nthawi zonse mu ntchito ya Ambuye,+ podziwa kuti zonse zimene mukuchita mu ntchito ya Ambuye sizidzapita pachabe.+
14 Pakuti kwenikweni timachita nawo zimene Khristu akuchita,+ ngati zinthu zimene tinali kudalira pa chiyambi, tazigwira mwamphamvu mpaka mapeto.+