Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 15:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma inuyo khalani olimba mtima+ ndipo musagwe ulesi,+ pakuti mudzapeza mphoto chifukwa cha ntchito yanu.”+

  • 1 Akorinto 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Choncho wobzala ndi wothirira ali amodzi,+ koma aliyense payekha adzalandira mphoto yake mogwirizana ndi ntchito yake.+

  • Chivumbulutso 14:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kenako ndinamva mawu kuchokera kumwamba akuti: “Lemba: Odala ndiwo anthu amene akufa+ mwa Ambuye+ kuyambira pa nthawi ino kupita m’tsogolo.+ Mzimu ukuti, alekeni akapumule ku ntchito yawo imene anaigwira mwakhama, pakuti zimene anachita zikupita nawo limodzi.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena