Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 14
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 14:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 1:29; Chv 5:6; 22:3
  • +Sl 2:6; Ahe 12:22; 1Pe 2:6
  • +Chv 7:4
  • +Chv 3:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 31

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2006, tsa. 5

    7/1/1995, tsa. 13

    12/15/1988, tsa. 20

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 198-200

Chivumbulutso 14:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:15
  • +2Mb 5:12; Chv 5:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 200

Chivumbulutso 14:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Mb 6:31
  • +Sl 33:3; 98:1; 149:1; Chv 5:9
  • +Chv 4:6
  • +Chv 4:4; 19:4
  • +Chv 7:4; 14:1
  • +1Ak 6:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 31

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 200-201, 202-203

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, tsa. 20

Chivumbulutso 14:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yak 1:27
  • +2Ak 11:2; Yak 4:4
  • +1Pe 2:21
  • +1Ak 7:23; Chv 5:9
  • +Eks 23:16; Le 23:15; Yak 1:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 24

    1/1/2007, tsa. 22

    2/15/2006, ptsa. 19-20

    6/1/1989, ptsa. 12-13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 201-203

Chivumbulutso 14:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 14:5; Chv 21:27
  • +Aef 5:27; Yuda 24

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 24

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 201-202

Chivumbulutso 14:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 4:11; Chv 8:13; 19:17
  • +Mt 24:14; Mko 13:10
  • +Mac 1:8; Akl 1:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    7/2022, tsa. 9

    5/2022, ptsa. 6-7

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 5

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/2007, tsa. 19

    12/15/2004, ptsa. 18-19

    12/1/1999, ptsa. 9-11

    11/1/1995, tsa. 8

    6/15/1992, ptsa. 14-15

    1/1/1990, tsa. 3

    12/15/1988, tsa. 20

    1/1/1988, tsa. 16

    5/15/1987, ptsa. 12-13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 203-205, 313

    Mphunzitsi Waluso, tsa. 65

Chivumbulutso 14:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 8:13; Mt 10:28
  • +Sl 19:1; Aro 11:36; Yuda 25; Chv 4:9
  • +1Pe 4:17; 2Pe 2:9
  • +Eks 20:11; Sl 124:8; 146:6
  • +Mac 14:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/2007, tsa. 19

    10/1/2005, ptsa. 23-25

    12/1/1999, ptsa. 10-11

    6/15/1998, tsa. 20

    1/1/1990, ptsa. 14-15

    1/1/1989, ptsa. 29-30

    12/15/1988, ptsa. 19-24

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 203-205

    Dikirani!, ptsa. 12-14

    Mphunzitsi Waluso, tsa. 65

    Sukulu ya Utumiki, ptsa. 272-275

Chivumbulutso 14:8

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto 7.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 17:18; 18:2
  • +Yes 21:9; Yer 51:8; Chv 18:21
  • +Yer 51:7
  • +Chv 17:2; 18:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 205-209, 245

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/2005, tsa. 24

    5/1/1989, ptsa. 3-5

    4/15/1989, ptsa. 4-9

    4/1/1989, tsa. 21

    12/15/1988, ptsa. 20-21

    1/1/1988, tsa. 16

    Yesaya 1, ptsa. 223-224

Chivumbulutso 14:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 13:1
  • +Chv 13:15
  • +Chv 13:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 209-210

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/2005, ptsa. 24-25

    1/1/1988, tsa. 16

Chivumbulutso 14:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 75:8; Chv 11:18; 16:19
  • +Chv 20:10
  • +Chv 21:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 209-211

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1993, tsa. 7

    Kukambitsirana, ptsa. 147-148

Chivumbulutso 14:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 25:46; 2At 1:9; Chv 19:3
  • +Chv 13:16; 16:2; 20:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 210-211

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1993, tsa. 7

    Kukambitsirana, ptsa. 147-148

Chivumbulutso 14:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 13:10
  • +Mla 12:13; Chv 1:3
  • +Ahe 10:38

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 210-211

Chivumbulutso 14:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Akl 3:3
  • +Aro 6:3; 1Ak 15:51
  • +1At 4:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 211

Chivumbulutso 14:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 7:13; Mt 25:31; Mac 1:11; Chv 1:7
  • +Sl 21:3; Chv 6:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 88-89

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2010, ptsa. 26-27

    12/15/1988, tsa. 21

    1/1/1988, tsa. 11

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 211

Chivumbulutso 14:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mko 4:29
  • +Mt 13:39
  • +Yow 3:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 88-89

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2010, ptsa. 26-27

    1/1/1988, tsa. 11

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 211-212

Chivumbulutso 14:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 88

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2010, ptsa. 26-27

    12/15/1988, tsa. 21

    1/1/1988, tsa. 11

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 211-212

Chivumbulutso 14:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 11:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 212

Chivumbulutso 14:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 20:9
  • +De 32:32

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 4

    6/1/1999, ptsa. 6-7

    1/1/1988, tsa. 18

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 212

Chivumbulutso 14:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 13:39; Chv 9:11
  • +Yer 12:10
  • +Chv 19:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 212-213, 215

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, tsa. 21

Chivumbulutso 14:20

Mawu a M'munsi

  • *

    Makilomita 296. “Sitadiya” ndi muyezo wakale wachigiriki woyezera mtunda. “Sitadiya” imodzi ndi yofanana ndi mamita 185.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ahe 13:12; Chv 22:15
  • +Miy 21:31
  • +Yer 25:33

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 212-214

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 14:1Yoh 1:29; Chv 5:6; 22:3
Chiv. 14:1Sl 2:6; Ahe 12:22; 1Pe 2:6
Chiv. 14:1Chv 7:4
Chiv. 14:1Chv 3:12
Chiv. 14:2Chv 1:15
Chiv. 14:22Mb 5:12; Chv 5:8
Chiv. 14:31Mb 6:31
Chiv. 14:3Sl 33:3; 98:1; 149:1; Chv 5:9
Chiv. 14:3Chv 4:6
Chiv. 14:3Chv 4:4; 19:4
Chiv. 14:3Chv 7:4; 14:1
Chiv. 14:31Ak 6:20
Chiv. 14:4Yak 1:27
Chiv. 14:42Ak 11:2; Yak 4:4
Chiv. 14:41Pe 2:21
Chiv. 14:41Ak 7:23; Chv 5:9
Chiv. 14:4Eks 23:16; Le 23:15; Yak 1:18
Chiv. 14:5Miy 14:5; Chv 21:27
Chiv. 14:5Aef 5:27; Yuda 24
Chiv. 14:6De 4:11; Chv 8:13; 19:17
Chiv. 14:6Mt 24:14; Mko 13:10
Chiv. 14:6Mac 1:8; Akl 1:23
Chiv. 14:7Miy 8:13; Mt 10:28
Chiv. 14:7Sl 19:1; Aro 11:36; Yuda 25; Chv 4:9
Chiv. 14:71Pe 4:17; 2Pe 2:9
Chiv. 14:7Eks 20:11; Sl 124:8; 146:6
Chiv. 14:7Mac 14:15
Chiv. 14:8Chv 17:18; 18:2
Chiv. 14:8Yes 21:9; Yer 51:8; Chv 18:21
Chiv. 14:8Yer 51:7
Chiv. 14:8Chv 17:2; 18:3
Chiv. 14:9Chv 13:1
Chiv. 14:9Chv 13:15
Chiv. 14:9Chv 13:16
Chiv. 14:10Sl 75:8; Chv 11:18; 16:19
Chiv. 14:10Chv 20:10
Chiv. 14:10Chv 21:8
Chiv. 14:11Mt 25:46; 2At 1:9; Chv 19:3
Chiv. 14:11Chv 13:16; 16:2; 20:4
Chiv. 14:12Chv 13:10
Chiv. 14:12Mla 12:13; Chv 1:3
Chiv. 14:12Ahe 10:38
Chiv. 14:13Akl 3:3
Chiv. 14:13Aro 6:3; 1Ak 15:51
Chiv. 14:131At 4:16
Chiv. 14:14Da 7:13; Mt 25:31; Mac 1:11; Chv 1:7
Chiv. 14:14Sl 21:3; Chv 6:2
Chiv. 14:15Mko 4:29
Chiv. 14:15Mt 13:39
Chiv. 14:15Yow 3:13
Chiv. 14:17Chv 11:19
Chiv. 14:18Chv 20:9
Chiv. 14:18De 32:32
Chiv. 14:19Mt 13:39; Chv 9:11
Chiv. 14:19Yer 12:10
Chiv. 14:19Chv 19:15
Chiv. 14:20Ahe 13:12; Chv 22:15
Chiv. 14:20Miy 21:31
Chiv. 14:20Yer 25:33
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 14:1-20

Chivumbulutso

14 Nditayang’ana, ndinaona Mwanawankhosa+ ataimirira paphiri la Ziyoni.+ Limodzi naye panali enanso 144,000+ olembedwa dzina lake ndi dzina la Atate+ wake pamphumi pawo. 2 Kenako ndinamva phokoso kumwamba ngati mkokomo wa madzi ambiri,+ ndiponso ngati phokoso la bingu lamphamvu. Phokoso ndinamvalo linali ngati la oimba amene akuimba motsagana ndi azeze awo.+ 3 Iwo anali kuimba+ nyimbo yokhala ngati yatsopano+ pamaso pa mpando wachifumu, pamaso pa zamoyo zinayi,+ ndi pamaso pa akulu.+ Palibe anatha kuiphunzira nyimboyo, koma 144,000+ amene anagulidwa+ padziko lapansi. 4 Awa ndiwo amene sanadziipitse ndi akazi,+ ndipo ali ngati anamwali.+ Amenewa ndiwo amatsatira Mwanawankhosa kulikonse kumene akupita.+ Iwowa anagulidwa+ kuchokera mwa anthu, monga zipatso zoyambirira+ zoperekedwa kwa Mulungu ndi kwa Mwanawankhosa. 5 M’kamwa mwawo simunapezeke chinyengo,+ ndipo alibe chilema.+

6 Ndinaona mngelo winanso akuuluka chapafupi m’mlengalenga.+ Iye anali ndi uthenga wabwino+ wosatha woti aulengeze monga nkhani yosangalatsa kwa anthu okhala padziko lapansi, ndi kudziko lililonse, fuko lililonse, chinenero chilichonse, ndi mtundu uliwonse.+ 7 Iye anali kunena mofuula kuti: “Opani Mulungu+ ndi kumupatsa ulemerero,+ chifukwa ola lakuti apereke chiweruzo lafika.+ Chotero lambirani Iye amene anapanga+ kumwamba, dziko lapansi, nyanja, ndi akasupe amadzi.”+

8 Kenako mngelo wina wachiwiri anamutsatira, ndipo anati: “Wagwa! Babulo+ Wamkulu wagwa,+ amene anachititsa mitundu yonse ya anthu kumwako vinyo+ wa mkwiyo wake ndi wa dama* lake!”+

9 Mngelo wina wachitatu anawatsatira, ndipo ananena mofuula kuti: “Ngati wina walambira chilombo+ ndi chifaniziro chake,+ ndipo walandira chizindikiro pamphumi kapena padzanja lake,+ 10 adzamwanso vinyo wosasungunula wa mkwiyo+ wa Mulungu amene akuthiridwa m’kapu ya mkwiyo wake. Ndipo adzazunzidwa+ ndi moto ndi sulufule+ pamaso pa angelo oyera, ndi pamaso pa Mwanawankhosa. 11 Ndipo utsi wa kuzunzidwa kwawo udzafuka kwamuyaya.+ Amene anali kulambira chilombo ndi chifaniziro chake, ndiponso aliyense amene walandira chizindikiro+ cha dzina lake, sadzapuma usana ndi usiku. 12 Kwa oyerawo,+ amene akusunga malamulo a Mulungu+ ndi kutsatira chikhulupiriro+ cha Yesu, apa ndiye pofunika kupirira.”

13 Kenako ndinamva mawu kuchokera kumwamba akuti: “Lemba: Odala ndiwo anthu amene akufa+ mwa Ambuye+ kuyambira pa nthawi ino kupita m’tsogolo.+ Mzimu ukuti, alekeni akapumule ku ntchito yawo imene anaigwira mwakhama, pakuti zimene anachita zikupita nawo limodzi.”

14 Nditayang’ana, ndinaona mtambo woyera. Pamtambopo panakhala winawake ngati mwana wa munthu,+ atavala chisoti chachifumu chagolide+ kumutu kwake, chikwakwa chakuthwa chili m’dzanja lake.

15 Mngelo wina anatuluka m’nyumba yopatulika ya pakachisi, akufuula kwa wokhala pamtambo uja ndi mawu okweza, kuti: “Tsitsa chikwakwa chako ndi kuyamba kumweta,+ chifukwa ola la kumweta lafika.+ Pakuti zokolola za padziko lapansi zapsa bwino.”+ 16 Choncho wokhala pamtambo uja anatsitsira chikwakwa chake chija kudziko lapansi mwamphamvu, ndipo anamweta dziko lapansi.

17 Mngelo winanso anatuluka m’nyumba yopatulika ya pakachisi amene ali kumwamba,+ nayenso ali ndi chikwakwa chakuthwa.

18 Ndipo mngelo winanso anatuluka kuguwa lansembe. Iyeyu anali ndi ulamuliro pa moto.+ Anafuula kwa mngelo amene anali ndi chikwakwa chakuthwa uja ndi mawu okweza, akuti: “Tsitsa chikwakwa chako chakuthwacho umwete mpesa wa padziko lapansi,+ ndi kusonkhanitsa pamodzi masango a mphesa zake, chifukwa mphesa zakezo zapsa.” 19 Mngeloyo+ anatsitsira chikwakwa chake kudziko lapansi mwamphamvu, ndi kumweta mpesa+ wa padziko lapansi. Ndiyeno anauponya m’choponderamo mphesa chachikulu cha mkwiyo wa Mulungu.+ 20 Ndipo anapondaponda mopondera mphesamo kunja kwa mzinda,+ ndipo magazi anatuluka m’choponderamo mphesacho mpaka kufika m’zibwano za mahatchi,+ n’kuyenderera mtunda wa masitadiya 1,600.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena