Ekisodo 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti m’masiku 6 Yehova anapanga kumwamba, dziko lapansi, nyanja, ndi zonse zili mmenemo,+ ndipo anayamba kupuma pa tsiku la 7.+ N’chifukwa chake Yehova anadalitsa tsiku la sabata ndi kulipanga kukhala lopatulika.+ Salimo 124:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Thandizo lathu lili m’dzina la Yehova,+Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi.”+ Salimo 146:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi,+Nyanja ndi zonse zili mmenemo.+Wosunga choonadi mpaka kalekale.+
11 Pakuti m’masiku 6 Yehova anapanga kumwamba, dziko lapansi, nyanja, ndi zonse zili mmenemo,+ ndipo anayamba kupuma pa tsiku la 7.+ N’chifukwa chake Yehova anadalitsa tsiku la sabata ndi kulipanga kukhala lopatulika.+
6 Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi,+Nyanja ndi zonse zili mmenemo.+Wosunga choonadi mpaka kalekale.+