Ekisodo 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa kwa masiku 6 Yehova anapanga kumwamba, dziko lapansi, nyanja ndiponso zonse zimene zili mmenemo ndipo anayamba kupuma pa tsiku la 7.+ Nʼchifukwa chake Yehova anadalitsa tsiku la Sabata ndipo analipanga kukhala lopatulika.
11 Chifukwa kwa masiku 6 Yehova anapanga kumwamba, dziko lapansi, nyanja ndiponso zonse zimene zili mmenemo ndipo anayamba kupuma pa tsiku la 7.+ Nʼchifukwa chake Yehova anadalitsa tsiku la Sabata ndipo analipanga kukhala lopatulika.