Genesis 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Pa chiyambi,+ Mulungu+ analenga+ kumwamba ndi dziko lapansi.+ Salimo 121:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Thandizo langa lichokera kwa Yehova,+Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi.+ Salimo 134:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova, amene ndiye Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi,+Akudalitseni ali ku Ziyoni.+ Machitidwe 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atamva zimenezi, onse pamodzi anafuula kwa Mulungu+ mokweza mawu kuti: “Ambuye Wamkulu Koposa,+ Inu ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zokhala mmenemo.+
24 Atamva zimenezi, onse pamodzi anafuula kwa Mulungu+ mokweza mawu kuti: “Ambuye Wamkulu Koposa,+ Inu ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zokhala mmenemo.+