Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti m’masiku 6 Yehova anapanga kumwamba, dziko lapansi, nyanja, ndi zonse zili mmenemo,+ ndipo anayamba kupuma pa tsiku la 7.+ N’chifukwa chake Yehova anadalitsa tsiku la sabata ndi kulipanga kukhala lopatulika.+

  • Nehemiya 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Inu ndinu Yehova, inu nokha.+ Ndinu amene munapanga kumwamba,+ ngakhale kumwambamwamba ndi makamu ake onse.+ Ndinu amene munapanga dziko lapansi+ ndi zonse zili momwemo+ komanso nyanja+ ndi zonse zili momwemo.+ Ndinu amene mukusunga zinthu zonse kuti zikhale ndi moyo. Ndipo makamu+ akumwamba amakugwadirani.

  • Salimo 146:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi,+

      Nyanja ndi zonse zili mmenemo.+

      Wosunga choonadi mpaka kalekale.+

  • Chivumbulutso 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iye analumbira pa Iye wokhala+ ndi moyo kwamuyaya,+ amene analenga kumwamba ndi zokhala kumeneko, ndi dziko lapansi+ ndi zinthu za mmenemo,+ ndi nyanja ndi zinthu za mmenemo. Analumbira kuti: “Sipakhalanso kuchedwa ayi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena