Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 46:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ine ndabweretsa pafupi chilungamo changa.+ Chilungamocho sichili kutali,+ ndipo chipulumutso changa sichidzachedwa.+ Ndidzapereka chipulumutso mu Ziyoni, ndipo Isiraeli ndidzam’patsa kukongola kwanga.”+

  • Ezekieli 12:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 ‘“Pakuti ine Yehova ndidzalankhula, ndipo mawu amene ndidzalankhulewo adzakwaniritsidwadi.+ Sindidzazengerezanso+ chifukwa ine ndidzalankhula mawu m’masiku anu,+ inu a m’nyumba yopanduka, ndipo mawuwo ndidzawakwaniritsa,” watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”

  • Habakuku 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Uchite zimenezi pakuti masomphenyawa akuyembekezera nthawi yake yoikidwiratu+ ndipo akuthamangira kumapeto kwake. Zimene zili m’masomphenyazi si zonama. Ngakhale masomphenyawa atazengereza, uziwayembekezerabe* chifukwa adzakwaniritsidwa ndithu.+ Iwo sadzachedwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena