Mika 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ine ndidzadikirira Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+ Yakobo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho lezani mtima abale, kufikira kukhalapo*+ kwa Ambuye. Ganizirani mmene amachitira mlimi. Iye amayembekezerabe zipatso zofunika kwambiri zotuluka m’nthaka. Amakhala wodekha mpaka itagwa mvula yoyamba ndi mvula yomaliza.+
7 Koma ine ndidzadikirira Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+
7 Choncho lezani mtima abale, kufikira kukhalapo*+ kwa Ambuye. Ganizirani mmene amachitira mlimi. Iye amayembekezerabe zipatso zofunika kwambiri zotuluka m’nthaka. Amakhala wodekha mpaka itagwa mvula yoyamba ndi mvula yomaliza.+