Genesis 49:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithu ndidzayembekezera chipulumutso kwa inu, Yehova.+ Salimo 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyendetseni m’choonadi chanu ndi kundiphunzitsa,+Pakuti inu ndinu Mulungu wa chipulumutso changa.+ ו [Waw]Chiyembekezo changa chili mwa inu tsiku lonse.+ Salimo 62:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Ndithudi, moyo wanga ukuyembekezera Mulungu modekha.+Chipulumutso changa chidzachokera kwa iye.+ Maliro 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndi bwino kuti munthu ayembekezere+ chipulumutso cha Yehova+ moleza mtima.+ Luka 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno mu Yerusalemu munali munthu wina dzina lake Simiyoni. Mwamuna ameneyu anali wolungama ndi woopa Mulungu. Anali kuyembekezera nthawi imene Mulungu adzatonthoze Isiraeli,+ ndipo mzimu woyera unali pa iye.
5 Ndiyendetseni m’choonadi chanu ndi kundiphunzitsa,+Pakuti inu ndinu Mulungu wa chipulumutso changa.+ ו [Waw]Chiyembekezo changa chili mwa inu tsiku lonse.+
25 Ndiyeno mu Yerusalemu munali munthu wina dzina lake Simiyoni. Mwamuna ameneyu anali wolungama ndi woopa Mulungu. Anali kuyembekezera nthawi imene Mulungu adzatonthoze Isiraeli,+ ndipo mzimu woyera unali pa iye.