Salimo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chipulumutso chimachokera kwa Yehova.+Madalitso anu ali pa anthu anu.+ [Seʹlah.] Salimo 37:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya nsautso.+ Salimo 68:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Adalitsike Yehova, amene amanyamula katundu wathu tsiku ndi tsiku,+Mulungu woona wa chipulumutso chathu.+ [Seʹlah.] Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+
39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya nsautso.+
19 Adalitsike Yehova, amene amanyamula katundu wathu tsiku ndi tsiku,+Mulungu woona wa chipulumutso chathu.+ [Seʹlah.]
2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+