Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 37:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+

      Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya nsautso.+

  • Miyambo 21:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Hatchi* anaikonzera tsiku la nkhondo,+ koma Yehova ndiye amapulumutsa.+

  • Yesaya 43:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ine ndine Yehova.+ Popanda ine palibenso mpulumutsi wina.”+

  • Hoseya 13:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Koma ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+ Panalibe Mulungu wina amene unali kumudziwa kupatulapo ine. Panalibenso mpulumutsi wina kupatulapo ine.+

  • Yona 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Koma ine, ndidzakutamandani ndi kupereka nsembe kwa inu.+

      Zimene ndalonjeza ndidzazikwaniritsa.+ Chipulumutso chimachokera kwa Yehova.”+

  • Chivumbulutso 19:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Zimenezi zitatha, ndinamva mawu ofuula kumwamba+ ngati mawu a khamu lalikulu, akuti: “Tamandani Ya,* anthu inu!+ Chipulumutso,+ ulemerero, ndi mphamvu ndi za Mulungu wathu,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena