Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 20:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ulendo uno simufunikira kumenya nkhondo.+ Khalani m’malo anu, imani chilili+ ndi kuona Yehova akukupulumutsani.+ Inu Ayuda ndi anthu a ku Yerusalemu, musaope kapena kuchita mantha.+ Mawa mupite kukakumana nawo ndipo Yehova akhala nanu.’”+

  • Salimo 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Chipulumutso chimachokera kwa Yehova.+

      Madalitso anu ali pa anthu anu.+ [Seʹlah.]

  • Salimo 33:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Hatchi siingabweretse chipulumutso,+

      Siingapulumutse munthu chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+

  • Salimo 68:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Mulungu woona ndi Mulungu amene amatipulumutsa.+

      Ndipo njira zopulumukira ku imfa ndi za Yehova,+ Ambuye Wamkulu Koposa.+

  • Chivumbulutso 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iwo anapitirizabe kufuula ndi mawu okweza, kuti: “Chipulumutso chathu chachokera kwa Mulungu wathu,+ amene wakhala pampando wachifumu,+ ndi kwa Mwanawankhosa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena