Salimo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chipulumutso chimachokera kwa Yehova.+Madalitso anu ali pa anthu anu.+ [Seʹlah.] Luka 1:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Iye watikwezera ife nyanga*+ yachipulumutso m’nyumba ya mtumiki wake Davide, Tito 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 kapena kuwabera,+ koma akhale okhulupirika pa chilichonse,+ kuti akometsere chiphunzitso cha Mpulumutsi+ wathu Mulungu, m’zinthu zonse. Yuda 25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 kwa iyeyo, Mulungu yekhayo amenenso ndi Mpulumutsi wathu+ mwa Yesu Khristu+ Ambuye wathu, kukhale ulemerero,+ ukulu, mphamvu+ ndi ulamuliro,+ kuchokera kalekale+ kufikira panopa, mpaka ku nthawi yonse yomka muyaya.+ Ame.+
10 kapena kuwabera,+ koma akhale okhulupirika pa chilichonse,+ kuti akometsere chiphunzitso cha Mpulumutsi+ wathu Mulungu, m’zinthu zonse.
25 kwa iyeyo, Mulungu yekhayo amenenso ndi Mpulumutsi wathu+ mwa Yesu Khristu+ Ambuye wathu, kukhale ulemerero,+ ukulu, mphamvu+ ndi ulamuliro,+ kuchokera kalekale+ kufikira panopa, mpaka ku nthawi yonse yomka muyaya.+ Ame.+