Salimo 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova adzapatsa anthu ake mphamvu.+Yehova adzadalitsa anthu ake ndi mtendere.+ Aefeso 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atamandike Mulungu, Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu,+ pakuti watidalitsa+ ndi dalitso lililonse lauzimu m’malo akumwamba+ mogwirizana ndi Khristu. Aheberi 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anati: “Kudalitsa, ndidzakudalitsa ndithu, ndipo ndidzakuchulukitsadi.”+
3 Atamandike Mulungu, Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu,+ pakuti watidalitsa+ ndi dalitso lililonse lauzimu m’malo akumwamba+ mogwirizana ndi Khristu.