Aefeso 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ndipo anatikweza+ pamodzi, ndi kutikhazika pamodzi m’malo akumwamba+ mogwirizana ndi Khristu Yesu.